-
Oweruza 7:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndikakaliza lipenga la nyanga ya nkhosa pamodzi ndi anthu onse a mʼgulu langa, nanunso mukalize malipenga anu kuzungulira msasa wonse, ndipo mukafuule kuti, ‘Nkhondo ya Yehova ndi ya Gidiyoni!’”
-