-
Oweruza 8:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Koma akalonga a ku Sukoti anayankha kuti: “Tipatse asilikali ako mkate chifukwa chiyani? Wagwira kale Zeba ndi Zalimuna?”
-