Oweruza 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atatero Gidiyoni anawauza kuti: “Chifukwa cha zimene mwanenazi, Yehova akapereka Zeba ndi Zalimuna mʼmanja mwanga, ndidzakukwapulani ndi mitengo yaminga yamʼchipululu komanso ndi zitsamba zaminga.”+
7 Atatero Gidiyoni anawauza kuti: “Chifukwa cha zimene mwanenazi, Yehova akapereka Zeba ndi Zalimuna mʼmanja mwanga, ndidzakukwapulani ndi mitengo yaminga yamʼchipululu komanso ndi zitsamba zaminga.”+