-
Oweruza 8:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Atachoka kumeneko anapita ku Penueli ndipo anawapemphanso chimodzimodzi, koma amuna a ku Penueli anamuyankha ngati mmene amuna a ku Sukoti aja anamuyankhira.
-