Oweruza 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Gidiyoni anapitirizabe ulendo wake ndipo anadutsa njira ya anthu okhala mʼmatenti, kumʼmawa kwa Noba ndi Yogebeha+ ndipo anaukira msasa wa adaniwo iwo asanakonzekere.
11 Gidiyoni anapitirizabe ulendo wake ndipo anadutsa njira ya anthu okhala mʼmatenti, kumʼmawa kwa Noba ndi Yogebeha+ ndipo anaukira msasa wa adaniwo iwo asanakonzekere.