Oweruza 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho, Gidiyoni anapita kwa amuna amumzinda wa Sukoti nʼkuwauza kuti: “Zeba ndi Zalimuna aja si awa? Amene munandinyoza nawo aja kuti, ‘Ukuti tipatse anyamata ako otopawo mkate chifukwa chiyani? Wagwira kale Zeba ndi Zalimuna?’”+
15 Choncho, Gidiyoni anapita kwa amuna amumzinda wa Sukoti nʼkuwauza kuti: “Zeba ndi Zalimuna aja si awa? Amene munandinyoza nawo aja kuti, ‘Ukuti tipatse anyamata ako otopawo mkate chifukwa chiyani? Wagwira kale Zeba ndi Zalimuna?’”+