-
Oweruza 8:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Gidiyoni anafunsa Zeba ndi Zalimuna kuti: “Kodi amuna amene munapha ku Tabori anali otani?” Iwo anayankha kuti: “Anali ngati iweyo. Aliyense ankaoneka ngati mwana wa mfumu.”
-