-
Oweruza 8:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Iwo anayankha kuti: “Tikupatsani.” Atatero anayala mkanjo, ndipo aliyense anaponyapo ndolo yapamphuno kuchokera pa zimene anatenga kunkhondo.
-