Oweruza 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Gidiyoni atangomwalira, Aisiraeli anayambanso kulambira Abaala,+ moti anaika Baala-beriti kukhala mulungu wawo.+
33 Gidiyoni atangomwalira, Aisiraeli anayambanso kulambira Abaala,+ moti anaika Baala-beriti kukhala mulungu wawo.+