Oweruza 8:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 ndipo sanasonyeze chikondi chokhulupirika kwa anthu a mʼbanja la Yerubaala, kapena kuti Gidiyoni, pa zabwino zonse zimene iye anachitira Isiraeli.+
35 ndipo sanasonyeze chikondi chokhulupirika kwa anthu a mʼbanja la Yerubaala, kapena kuti Gidiyoni, pa zabwino zonse zimene iye anachitira Isiraeli.+