-
Oweruza 9:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Koma mtengo wa maoliviwo unayankha kuti, ‘Kodi ndisiye kutulutsa mafuta amene amawagwiritsa ntchito potamanda Mulungu ndi anthu nʼkupita kuti ndizikagwedezeka pamwamba pa mitengo ina?’
-