Oweruza 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi mukuona kuti mwachita bwino kuika Abimeleki kukhala mfumu?+ Kodi mwachita zimenezi kuchokera pansi pa mtima? Nanga Yerubaala ndi banja lake mwamuchitira zabwino? Kodi zimene mwamuchitira ndi zogwirizana ndi zimene iye anachita?
16 Kodi mukuona kuti mwachita bwino kuika Abimeleki kukhala mfumu?+ Kodi mwachita zimenezi kuchokera pansi pa mtima? Nanga Yerubaala ndi banja lake mwamuchitira zabwino? Kodi zimene mwamuchitira ndi zogwirizana ndi zimene iye anachita?