Oweruza 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma inu lero mwaukira banja la bambo anga ndipo mwapha ana awo aamuna 70 pamwala umodzi.+ Kenako mwaika Abimeleki, mwana wa kapolo wake wamkazi,+ kukhala mfumu ya atsogoleri a ku Sekemu chifukwa chongoti ndi mchimwene wanu.
18 Koma inu lero mwaukira banja la bambo anga ndipo mwapha ana awo aamuna 70 pamwala umodzi.+ Kenako mwaika Abimeleki, mwana wa kapolo wake wamkazi,+ kukhala mfumu ya atsogoleri a ku Sekemu chifukwa chongoti ndi mchimwene wanu.