-
Oweruza 9:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ngati mwachitira zimenezi Yerubaala kuchokera pansi pa mtima ndipo mukuona kuti mwachita bwino, sangalalani ndi Abimeleki ndipo nayenso asangalale nanu.
-