-
Oweruza 9:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Gaala ataona anthuwo, anauza Zebuli kuti: “Taona, kukubwera anthu kuchokera pamwamba pa mapiri.” Koma Zebuli anati: “Si anthu amenewo, ukuona zithunzithunzi za mapiri.”
-