-
Oweruza 9:48Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
48 iye limodzi ndi anthu onse amene anali naye anapita kuphiri la Zalimoni. Abimeleki anatenga nkhwangwa, ndipo anadula nthambi ya mtengo nʼkuinyamula paphewa. Kenako anauza anthu amene anali naye kuti: “Zimene mwaona ine ndikuchita, inunso muchite zomwezo mofulumira!”
-