-
Oweruza 9:51Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
51 Pakati pa mzindawo panali nsanja yolimba ndipo amuna ndi akazi onse komanso atsogoleri onse amumzindawo, anathawira munsanjayo. Atalowa mmenemo, anatseka chitseko nʼkukwera padenga la nsanjayo.
-