Oweruza 9:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Mulungu anachititsanso kuti zoipa zonse za amuna a ku Sekemu ziwabwerere pamutu pawo. Choncho zimene Yotamu mwana wa Yerubaala+ ananena powatemberera,+ zinakwaniritsidwa.
57 Mulungu anachititsanso kuti zoipa zonse za amuna a ku Sekemu ziwabwerere pamutu pawo. Choncho zimene Yotamu mwana wa Yerubaala+ ananena powatemberera,+ zinakwaniritsidwa.