Oweruza 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Abimeleki atafa, panabwera Tola, mwana wa Puwa amene anali mwana wa Dodo wa fuko la Isakara ndipo anapulumutsa Isiraeli.+ Iye ankakhala ku Samiri mʼdera lamapiri la Efuraimu.
10 Abimeleki atafa, panabwera Tola, mwana wa Puwa amene anali mwana wa Dodo wa fuko la Isakara ndipo anapulumutsa Isiraeli.+ Iye ankakhala ku Samiri mʼdera lamapiri la Efuraimu.