Oweruza 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Patapita nthawi, Aamoni+ anasonkhana nʼkumanga msasa wawo ku Giliyadi. Zitatero, Aisiraeli nawonso anasonkhana nʼkumanga msasa wawo ku Mizipa.
17 Patapita nthawi, Aamoni+ anasonkhana nʼkumanga msasa wawo ku Giliyadi. Zitatero, Aisiraeli nawonso anasonkhana nʼkumanga msasa wawo ku Mizipa.