Oweruza 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Yefita anauza akulu a ku Giliyadiwo kuti: “Kodi si inu amene munkadana nane kwambiri mpaka kundithamangitsa mʼnyumba ya bambo anga?+ Ndiye lero mwandifuna chifukwa choti mwakumana ndi mavuto?”
7 Koma Yefita anauza akulu a ku Giliyadiwo kuti: “Kodi si inu amene munkadana nane kwambiri mpaka kundithamangitsa mʼnyumba ya bambo anga?+ Ndiye lero mwandifuna chifukwa choti mwakumana ndi mavuto?”