Oweruza 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Akulu a ku Giliyadi anayankha Yefita kuti: “Zoona, nʼchifukwa chake tabwera kwa iwe. Ngati ungapite nafe kukamenyana ndi Aamoni, ukhala mtsogoleri wathu ku Giliyadi konse.”+
8 Akulu a ku Giliyadi anayankha Yefita kuti: “Zoona, nʼchifukwa chake tabwera kwa iwe. Ngati ungapite nafe kukamenyana ndi Aamoni, ukhala mtsogoleri wathu ku Giliyadi konse.”+