Oweruza 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 chifukwa atachoka ku Iguputo anadutsa mʼchipululu kukafika ku Nyanja Yofiira+ mpaka ku Kadesi.+