-
Oweruza 12:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ibizani anali ndi ana aamuna 30 ndi ana aakazi 30. Iye anakonza zoti ana ake aakazi akwatiwe ndi amuna a mafuko ena komanso anatuma anthu kukatenga atsikana 30 kuchokera kwina kuti akhale akazi a ana ake aamuna. Ibizani anaweruza Isiraeli kwa zaka 7.
-