Oweruza 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako mkaziyo anapita kukauza mwamuna wake kuti: “Munthu wa Mulungu woona anabwera kwa ine, ndipo amaoneka ngati mngelo wa Mulungu woona, amaoneka mochititsa mantha kwambiri. Koma sindinamʼfunse kumene wachokera ndiponso sanandiuze dzina lake.+
6 Kenako mkaziyo anapita kukauza mwamuna wake kuti: “Munthu wa Mulungu woona anabwera kwa ine, ndipo amaoneka ngati mngelo wa Mulungu woona, amaoneka mochititsa mantha kwambiri. Koma sindinamʼfunse kumene wachokera ndiponso sanandiuze dzina lake.+