-
Oweruza 13:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Mulungu woona anamva zimene Manowa anapempha, moti mngelo wa Mulungu woona uja anabweranso kwa mkaziyo, ndipo anamʼpeza atakhala pansi panja. Pa nthawiyi sanali limodzi ndi mwamuna wake Manowa.
-