Oweruza 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Asadye chilichonse chochokera ku mphesa, asamwe vinyo kapena chakumwa chilichonse choledzeretsa+ komanso asadye chilichonse chodetsedwa.+ Atsatire zonse zimene ndamuuza.”
14 Asadye chilichonse chochokera ku mphesa, asamwe vinyo kapena chakumwa chilichonse choledzeretsa+ komanso asadye chilichonse chodetsedwa.+ Atsatire zonse zimene ndamuuza.”