Oweruza 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano Manowa anauza mngelo wa Yehova kuti: “Dikirani pangʼono tikukonzereni kamwana ka mbuzi.”+