-
Oweruza 13:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Kenako Manowa anatenga kamwana ka mbuzi ndi nsembe yambewu nʼkuzipereka nsembe kwa Yehova pathanthwe. Pamene ankachita zimenezi, Mulungu ankachita zodabwitsa Manowa ndi mkazi wake akuona.
-