-
Oweruza 13:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Pamene malawi a moto ankakwera mʼmwamba kuchokera paguwa lansembelo, mngelo wa Yehova nayenso anakwera kumwamba mʼmalawi a motowo, Manowa ndi mkazi wake akuona. Nthawi yomweyo anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi.
-