Oweruza 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zitatero Manowa anadziwa kuti anali mngelo wa Yehova.+ Mngelo wa Yehovayo sanaonekerenso kwa Manowa ndi mkazi wake.
21 Zitatero Manowa anadziwa kuti anali mngelo wa Yehova.+ Mngelo wa Yehovayo sanaonekerenso kwa Manowa ndi mkazi wake.