Oweruza 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Patapita nthawi, Samisoni anabwerera kwa mkaziyo kuti akamʼtenge kupita naye kwawo.+ Ali mʼnjira, anapatuka kuti aone mkango umene anapha uja. Atafika anapeza kuti mkati mwa mkango wakufawo muli njuchi ndi uchi.
8 Patapita nthawi, Samisoni anabwerera kwa mkaziyo kuti akamʼtenge kupita naye kwawo.+ Ali mʼnjira, anapatuka kuti aone mkango umene anapha uja. Atafika anapeza kuti mkati mwa mkango wakufawo muli njuchi ndi uchi.