-
Oweruza 14:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndiyeno anatengako uchiwo mʼmanja nʼkumadya akuyenda. Atapezananso ndi bambo ndi mayi ake, anawagawira uchiwo kuti nawonso adye. Koma sanawauze kuti uchiwo wautenga mkati mwa mkango wakufa.
-