-
Oweruza 14:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Kenako Samisoni anawauza kuti: “Ndikufuna ndikuuzeni mwambi. Mukandiuza tanthauzo lake mʼmasiku 7 a phwandoli, ndidzakupatsani malaya 30 ndi zovala zina 30.
-