Oweruza 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la 4 anauza mkazi wa Samisoni kuti: “Umunyengerere mwamuna wako+ kuti atiuze tanthauzo la mwambiwu. Akapanda kutiuza, tikuwotcha ndi moto pamodzi ndi nyumba ya bambo ako. Kodi mwatiitana kuti mudzatilande katundu wathu?”
15 Pa tsiku la 4 anauza mkazi wa Samisoni kuti: “Umunyengerere mwamuna wako+ kuti atiuze tanthauzo la mwambiwu. Akapanda kutiuza, tikuwotcha ndi moto pamodzi ndi nyumba ya bambo ako. Kodi mwatiitana kuti mudzatilande katundu wathu?”