Oweruza 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mnyamata ameneyu anachoka mumzinda wa Betelehemu wa ku Yuda, kuti akapeze malo okhala. Ali pa ulendowu, anafika mʼdera lamapiri la Efuraimu, kunyumba ya Mika.+
8 Mnyamata ameneyu anachoka mumzinda wa Betelehemu wa ku Yuda, kuti akapeze malo okhala. Ali pa ulendowu, anafika mʼdera lamapiri la Efuraimu, kunyumba ya Mika.+