-
Oweruza 17:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndiyeno Mika anamʼfunsa kuti: “Wachokera kuti?” Iye anayankha kuti: “Ndine Mlevi, ndachokera ku Betelehemu wa ku Yuda ndipo ndikufufuza malo okhala.”
-