Oweruza 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamene ankayandikira nyumba ya Mika anamva Mlevi wachinyamata uja akulankhula ndipo anazindikira mawu ake.* Choncho anapita kunyumbako nʼkumufunsa kuti: “Wabwera ndi ndani kuno ndipo ukudzatani? Ukufunako chiyani kuno?”
3 Pamene ankayandikira nyumba ya Mika anamva Mlevi wachinyamata uja akulankhula ndipo anazindikira mawu ake.* Choncho anapita kunyumbako nʼkumufunsa kuti: “Wabwera ndi ndani kuno ndipo ukudzatani? Ukufunako chiyani kuno?”