Oweruza 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mukakafika, mukapeza anthu okhala mosatekeseka,+ ndipo malo ake ndi aakulu kwambiri. Malo amenewa ndi osasowa kalikonse kopezeka padziko lapansi ndipo Mulungu wakupatsani.”+
10 Mukakafika, mukapeza anthu okhala mosatekeseka,+ ndipo malo ake ndi aakulu kwambiri. Malo amenewa ndi osasowa kalikonse kopezeka padziko lapansi ndipo Mulungu wakupatsani.”+