Oweruza 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthuwa anayenda nʼkukamanga msasa ku Kiriyati-yearimu+ ku Yuda. Nʼchifukwa chake malo amenewa, omwe ali kumadzulo kwa Kiriyati-yearimu, amadziwika kuti Mahane-dani*+ mpaka lero.
12 Anthuwa anayenda nʼkukamanga msasa ku Kiriyati-yearimu+ ku Yuda. Nʼchifukwa chake malo amenewa, omwe ali kumadzulo kwa Kiriyati-yearimu, amadziwika kuti Mahane-dani*+ mpaka lero.