Oweruza 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho anakhotera kumeneko nʼkufika panyumba ya Mlevi wachinyamata uja,+ kunyumba ya Mika, ndipo anayamba kumufunsa za moyo wake.
15 Choncho anakhotera kumeneko nʼkufika panyumba ya Mlevi wachinyamata uja,+ kunyumba ya Mika, ndipo anayamba kumufunsa za moyo wake.