Oweruza 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pa nthawiyi nʼkuti amuna 600 okhala ndi zida zankhondo, a fuko la Dani+ aja, ataima pageti.