Oweruza 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Wansembeyo anagwirizana nazo ndipo anatenga efodi, aterafi* ndi chifaniziro chosema+ nʼkunyamuka ndi anthuwo.
20 Wansembeyo anagwirizana nazo ndipo anatenga efodi, aterafi* ndi chifaniziro chosema+ nʼkunyamuka ndi anthuwo.