Oweruza 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iwo analibe owalanditsa chifukwa mzindawo unali kutali ndi Sidoni ndipo sankayenderana ndi anthu ena. Komanso mzindawo unali mʼchigwa cha Beti-rehobu.+ Choncho anthu a fuko la Dani anamanganso mzindawo nʼkumakhalamo.
28 Iwo analibe owalanditsa chifukwa mzindawo unali kutali ndi Sidoni ndipo sankayenderana ndi anthu ena. Komanso mzindawo unali mʼchigwa cha Beti-rehobu.+ Choncho anthu a fuko la Dani anamanganso mzindawo nʼkumakhalamo.