Oweruza 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pa nthawi imene mu Isiraeli munalibe mfumu,+ Mlevi wina amene ankakhala mʼdera lamapiri lakutali kwambiri la Efuraimu,+ anakwatira wantchito wake wa ku Betelehemu,+ ku Yuda.
19 Pa nthawi imene mu Isiraeli munalibe mfumu,+ Mlevi wina amene ankakhala mʼdera lamapiri lakutali kwambiri la Efuraimu,+ anakwatira wantchito wake wa ku Betelehemu,+ ku Yuda.