-
Oweruza 19:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Choncho anakhala pansi ndipo onse awiri anayamba kudya ndi kumwa. Kenako bambo a mtsikanayo anauza mwamunayo kuti: “Bwanji lero mugone mupite mawa, ndipo musangalale?”
-