-
Oweruza 19:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Atadzuka mʼmawa tsiku la 5 kuti azipita, bambo a mtsikanayo anati: “Muyambe mwadya kaye kuti mupeze mphamvu.” Choncho iwo anakhalabe mpaka chakumadzulo, ndipo onse awiri anapitirizabe kudya.
-