Oweruza 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atafika mumzinda wa Gibeya, anaima kuti agone mmenemo ndipo anakhala pabwalo la mzindawo. Koma palibe amene anawatenga kuti akagone kunyumba kwake.+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:15 Nsanja ya Olonda,1/15/2005, tsa. 27
15 Atafika mumzinda wa Gibeya, anaima kuti agone mmenemo ndipo anakhala pabwalo la mzindawo. Koma palibe amene anawatenga kuti akagone kunyumba kwake.+