-
Oweruza 19:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Atakweza maso, anaona mwamuna wapaulendo uja ali mʼbwalo la mzinda. Ndiyeno bambo wachikulireyo anamufunsa kuti: “Ukupita kuti, nanga ukuchokera kuti?”
-