-
Oweruza 19:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Koma bambo wachikulireyo anati: “Mtendere ukhale nawe! Ine ndikupatsa chilichonse chimene ungafunikire. Koma usagone pabwalo la mzindali.”
-